2 Mbiri 13:22 - Buku Lopatulika22 Machitidwe ena tsono a Abiya, ndi mayendedwe ake, ndi mau ake, alembedwa m'buku lomasulira la mneneri Ido. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Machitidwe ena tsono a Abiya, ndi mayendedwe ake, ndi mau ake, alembedwa m'buku lomasulira la mneneri Ido. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Ntchito zonse za Abiya, makhalidwe ake ndi zimene ankalankhula zidalembedwa m'buku la mbiri ya mneneri Ido. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Zina ndi zina zokhudza Abiya, zimene anachita ndi zimene anayankhula, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mneneri Ido. Onani mutuwo |