Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 13:16 - Buku Lopatulika

16 Ndipo ana a Israele anathawa pamaso pa Yuda, nawapereka Mulungu m'dzanja lao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndipo ana a Israele anathawa pamaso pa Yuda, nawapereka Mulungu m'dzanja lao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Aisraele adathaŵa Ayuda, ndipo Mulungu adapereka Aisraelewo kwa Ayuda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Aisraeli anathawa Ayuda. Ndipo Mulungu anawapereka mʼmanja mwawo.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 13:16
10 Mawu Ofanana  

ayamikike Mulungu Wamkulukulu amene wapereka adani ako m'dzanja lako. Ndipo anampatsa iye limodzi la magawo khumi la zonse.


Ndipo Abiya ndi anthu ake anawakantha makanthidwe aakulu; nagwa, nafa amuna osankhika zikwi mazana asanu a Israele.


Nanga Akusi ndi Alibiya, sanakhale khamu lalikulukulu, ndi magaleta ndi apakavalo ambirimbiri, koma muja munatama Yehova anawapereka m'dzanja mwanu?


Kuyambira ku Aroere, ndiko kumphepete kwa mtsinje wa Arinoni, ndi kumudzi wokhala kumtsinje kufikira ku Giliyadi, kunalibe mzinda wakutitalikira malinga ake; Yehova Mulungu wathu anapereka yonse pamaso pathu.


Potero Yehova Mulungu wathu anaperekanso m'manja mwathu Ogi mfumu ya Basani, ndi anthu ake onse, ndipo tinamkantha kufikira sanamtsalire ndi mmodzi yense.


Pomwepo Yoswa ananena kwa Yehova tsiku limene Yehova anapereka Aamori pamaso pa ana a Israele; ndipo anati pamaso pa Israele, Dzuwa iwe, linda, pa Gibiyoni, ndi Mwezi iwe, m'chigwa cha Ayaloni.


Ndipo Yehova anawapatsa mpumulo pozungulira ponse, monga mwa zonse adalumbirira makolo ao; ndipo pamaso pao sipanaime munthu mmodzi wa adani ao onse; Yehova anapereka adani ao onse m'manja mwao.


Ndipo Yuda atakwera, Yehova anapereka Akanani ndi Aperizi m'dzanja lao, ndipo anakantha a iwowa anthu zikwi khumi ku Bezeki.


Ndipo Yehova Mulungu wa Israele anapereka Sihoni ndi anthu ake onse m'dzanja la Israele, ndipo anawakantha, ndi Israele, analandira cholowa chake, dziko lonse la Aamori, nzika za m'dziko lija.


Ndipo anthu anauza Saulo kuti Davide wafika ku Keila. Ndipo Saulo anati, Mulungu wampereka m'dzanja langa; pakuti atsekerezeka, popeza analowa m'mudzi wa zitseko ndi mipiringidzo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa