2 Mbiri 13:13 - Buku Lopatulika13 Koma Yerobowamu anazunguliritsa owalalira, awadzere kumbuyo; momwemo iwowa anali kumaso kwa Yuda, ndi owalalira anali kumbuyo kwao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Koma Yerobowamu anazunguliritsa owalalira, awadzere kumbuyo; momwemo iwowa anali kumaso kwa Yuda, ndi owalalira anali kumbuyo kwao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Yerobowamu anali atatumiza anthu obisalira, kuti alimbane nawo moŵadzera kumbuyo. Motero magulu ankhondowo anali kutsogolo kwa anthu a ku Yuda, ndipo obisalirawo anali kumbuyo kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Tsono Yeroboamu anali atatumiza asilikali kumbuyo mowazungulira, kotero kuti iye ali kutsogolo kwa anthu a ku Yuda, anthu owabisalira anali kumbuyo kwawo. Onani mutuwo |