Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Mbiri 13:1 - Buku Lopatulika

1 Ndipo chaka chakhumi mphambu zisanu ndi zitatu cha Yerobowamu, Abiya analowa ufumu wa Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo chaka chakhumi mphambu zisanu ndi zitatu cha Yerobowamu, Abiya analowa ufumu wa Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Pa chaka cha 18 cha ufumu wa Yerobowamu, Abiya adaloŵa ufumu wa ku Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Mʼchaka cha 18 cha ulamuliro wa Yeroboamu, Abiya analowa ufumu wa Yuda,

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 13:1
4 Mawu Ofanana  

Ndi pambuyo pake anatenga Maaka mwana wamkazi wa Abisalomu; ndipo anambalira Abiya, ndi Atai, ndi Ziza, ndi Selomiti.


Machitidwe ake tsono a Rehobowamu, zoyamba ndi zotsiriza, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a Semaya mneneriyo, ndi la Ido mlauliyo, lakunena za zibadwidwe? Ndipo panali nkhondo pakati pa Rehobowamu ndi Yerobowamu masiku onse.


Nagona Rehobowamu ndi makolo ake, naikidwa m'mzinda wa Davide; ndipo Abiya mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa