2 Mbiri 12:8 - Buku Lopatulika8 Koma adzakhala akapolo ake, kuti adziwe kunditumikira kwanga, ndi kuwatumikira kwa maufumu a maiko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma adzakhala akapolo ake, kuti adziwe kunditumikira kwanga, ndi kuwatumikira kwa maufumu a maiko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Komabe adzakhala akapolo a Sisakeyo, kuti anthuwo adziŵe kusiyanitsa pakati pa kutumikira Ine ndi kutumikira mafumu a maiko achilendo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Komabe iwo adzakhala pansi pa ulamuliro wake, kuti aphunzire kudziwa kusiyanitsa pakati pa kutumikira Ine ndi kutumikira mafumu a mayiko ena.” Onani mutuwo |