Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 12:16 - Buku Lopatulika

16 Nagona Rehobowamu ndi makolo ake, naikidwa m'mzinda wa Davide; ndipo Abiya mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Nagona Rehobowamu ndi makolo ake, naikidwa m'mudzi wa Davide; ndipo Abiya mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Rehobowamu adamwalira, naikidwa m'manda mu mzinda wa Davide. Tsono Abiya mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Rehobowamu anamwalira, ndipo anayikidwa mʼmanda mu mzinda wa Davide. Ndipo mwana wake Abiya analowa ufumu mʼmalo wake.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 12:16
5 Mawu Ofanana  

Ndipo mwana wa Solomoni ndiye Rehobowamu, Abiya mwana wake, Asa mwana wake, Yehosafati mwana wake,


Ndi pambuyo pake anatenga Maaka mwana wamkazi wa Abisalomu; ndipo anambalira Abiya, ndi Atai, ndi Ziza, ndi Selomiti.


Ndipo chaka chakhumi mphambu zisanu ndi zitatu cha Yerobowamu, Abiya analowa ufumu wa Yuda.


ndi Solomoni anabala Rehobowamu; ndi Rehobowamu anabala Abiya; ndi Abiya anabala Asa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa