Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 12:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo kunatero kuti pakulowa mfumu m'nyumba ya Yehova, anadza olindirira, nazinyamula, nazibwezanso ku chipinda cha olindirira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo kunatero kuti pakulowa mfumu m'nyumba ya Yehova, anadza olindirira, nazinyamula, nazibwezanso ku chipinda cha olindirira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Tsono nthaŵi zonse mfumu ikamaloŵa m'Nyumba ya Chauta, alondawo ankatenga zishango, kenaka nkumazibwezera ku chipinda cha alonda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Nthawi ina iliyonse imene mfumu ikupita ku Nyumba ya Yehova, alonda amapita nayo atanyamula zishango, ndipo kenaka amakazibwezera ku chipinda cha alonda.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 12:11
3 Mawu Ofanana  

Ndipo kunachitika, pakulowa mfumu m'nyumba ya Yehova, olindirira aja anazinyamula, nabweranso nazo ku chipinda cha olindirirawo.


Ndipo Rehobowamu mfumu anapanga m'malo mwa izi zikopa zamkuwa, nazipereka m'manja mwa kapitao wa olindirira akusunga pakhomo pa nyumba ya mfumu.


Ndipo pakudzichepetsa iye mkwiyo wa Yehova unamchokera, kuti usamuononge konse; ndiponso munatsalira zokoma mu Yuda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa