2 Mbiri 11:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo Rehobowamu anakhala mu Yerusalemu, namanga mizinda yolimbikiramo mu Yuda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Rehobowamu anakhala m'Yerusalemu, namanga midzi yolimbikiramo m'Yuda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Rehobowamu ankakhala ku Yerusalemu, ndipo adamanga mizinda yamalinga ku Yuda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Rehobowamu amakhala mu Yerusalemu ndipo anamanga mizinda ya chitetezo iyi mu Yuda: Onani mutuwo |