2 Mbiri 11:2 - Buku Lopatulika2 Koma mau a Yehova anadza kwa Semaya munthu wa Mulunguyo, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Koma mau a Yehova anadza kwa Semaya munthu wa Mulunguyo, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Koma Chauta adadza kwa Semaya, m'meneri wake, namlamula kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma Yehova anayankhula ndi munthu wa Mulungu Semaya kuti, Onani mutuwo |
Ndipo anaika monga mwa chiweruzo cha Davide atate wake zigawo za ansembe ku utumiki wao, ndi Alevi ku udikiro wao, kulemekeza Mulungu, ndi kutumikira pamaso pa ansembe, monga munayenera tsiku ndi tsiku; odikira omwe monga mwa zigawo zao ku chipata chilichonse; pakuti momwemo Davide munthu wa Mulungu adamuuza.