2 Mbiri 11:17 - Buku Lopatulika17 Momwemo analimbikitsa ufumu wa Yuda, nalimbikitsa Rehobowamu, mwana wa Solomoni zaka zitatu; pakuti anayenda m'njira ya Davide ndi Solomoni zaka zitatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Momwemo analimbikitsa ufumu wa Yuda, nalimbikitsa Rehobowamu, mwana wa Solomoni zaka zitatu; pakuti anayenda m'njira ya Davide ndi Solomoni zaka zitatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Iwowo adalimbitsa ufumu wa Yuda, ndipo adamsunga Rehobowamu mwana wa Solomoni zaka zitatu, chifukwa chakuti pa zaka zitatuzo ankatsata chitsanzo cha Davide ndi cha Solomoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Iwo analimbikitsa ufumu wa Yuda, ndipo anathandiza Rehobowamu mwana wa Solomoni kwa zaka zitatu. Pa nthawi imeneyi iye amatsatira zochita za Davide ndi Solomoni. Onani mutuwo |