2 Mbiri 11:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo analimbitsa malingawo, naikamo atsogoleri, ndi chakudya chosungikiratu, ndi mafuta, ndi vinyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo analimbitsa malingawo, naikamo atsogoleri, ndi chakudya chosungikiratu, ndi mafuta, ndi vinyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Malinga ake adamanga olimba, ndipo adaikamo atsogoleri a nkhondo. Adaikamonso chakudya, mafuta ndi vinyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Iye anakhwimitsa chitetezo cha mizindayi ndipo anayikamo atsogoleri a ankhondo, pamodzi ndi chakudya, mafuta a olivi ndi vinyo. Onani mutuwo |