2 Mbiri 11:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo atafika ku Yerusalemu Rehobowamu, anamemeza a nyumba ya Yuda ndi Benjamini amuna osankhika zikwi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu, ndiwo ankhondo, alimbane ndi Aisraele kubwezanso ufumu kwa Rehobowamu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo atafika ku Yerusalemu Rehobowamu, anamemeza a nyumba ya Yuda ndi Benjamini amuna osankhika zikwi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu, ndiwo ankhondo, alimbane ndi Aisraele kubwezanso ufumu kwa Rehobowamu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Rehobowamu atafika ku Yerusalemu, adasonkhanitsa ankhondo osankhidwa okwanira 180,000, afuko la Yuda ndi la Benjamini, ndi cholinga akamenyane nkhondo ndi anthu a ku Israele, kuti choncho ambwezere Rehobowamu ufumu wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Rehobowamu atafika ku Yerusalemu anasonkhanitsa asilikali 180,000 a fuko la Yuda ndi Benjamini kuti akachite nkhondo ndi Israeli, kuti abwezeretse ufumu kwa Rehobowamu. Onani mutuwo |