2 Mbiri 10:9 - Buku Lopatulika9 Nati nao, Mundipangire bwanji inu, kuti tibwezere mau anthu awa ananena nanewo, ndi kuti, Mupepuze goli limene atate wanu anatisenzetsa ife? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Nati nao, Mundipangire bwanji inu, kuti tibwezere mau anthu awa ananena nanewo, ndi kuti, Mupepuze goli limene atate wanu anatisenzetsa ife? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Adaŵafunsa kuti, “Kodi mungandilangize zotani kuti tiŵayankhe anthu ameneŵa amene andipempha kuti, ‘Tipeputsireniko goli limene bambo wanu adatisenzetsa?’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Iye anawafunsa kuti, “Kodi malangizo anu ndi otani? Kodi tiwayankhe chiyani anthu amene akunena kuti, ‘Peputsani goli limene abambo anu anayika pa ife?’ ” Onani mutuwo |