2 Mbiri 10:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo ananena naye, kuti, Mukawachitira chokoma anthu awa, ndi kuwakonda, ndi kulankhula nao mau okoma, adzakhala anyamata anu kosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo ananena naye, kuti, Mukawachitira chokoma anthu awa, ndi kuwakonda, ndi kulankhula nao mau okoma, adzakhala anyamata anu kosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Madodawo adamuuza kuti, “Mukaŵachitira chifundo anthu ameneŵa ndi kumaŵasangalatsa, mukalankhula nawo mau abwino, iwowo adzakutumikirani mpaka muyaya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iwo anayankha kuti, “Ngati inu muwakomera mtima anthu awa ndi kuwasangalatsa ndiponso kuwayankha mawu abwino, iwo adzakutumikirani nthawi zonse.” Onani mutuwo |