Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 10:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo ananena nao, Mubwerenso atapita masiku atatu. Nachoka anthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo ananena nao, Mubwerenso atapita masiku atatu. Nachoka anthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Rehobowamu adaŵauza kuti, “Mukabwerenso kuno patapita masiku atatu.” Choncho anthuwo adachoka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Rehobowamu anayankha kuti, “Mukabwerenso pakapita masiku atatu.” Choncho anthuwo anachoka.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 10:5
4 Mawu Ofanana  

Ndipo iye anati kwa iwo, Bamukani, mukagone masiku atatu, pamenepo mukabwera kwa ine. Ndipo anthu anamuka.


Atate wanu analemeretsa goli lathu; inu tsono pepuzaniko ntchito yolemetsa ya atate wanu, ndi goli lake lolemera anatisenzetsali, ndipo tidzakutumikirani.


Ndipo Rehobowamu mfumu anafunsana ndi akuluakulu, amene anaimirira pamaso pa Solomoni atate wake akali ndi moyo, nati, Mundipangire bwanji, kuti ndiwabwezere mau anthu awa?


Usanene kwa mnzako, Ukabwerenso, ndipo mawa ndidzakupatsa; pokhala uli nako kanthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa