2 Mbiri 10:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anatuma munthu kukamuitana, nadza Yerobowamu ndi Aisraele onse, nalankhula ndi Rehobowamu, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anatuma munthu kukamuitana, nadza Yerobowamu ndi Aisraele onse, nalankhula ndi Rehobowamu, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Anthu adakamuitana. Choncho Yerobowamu pamodzi ndi Aisraele onse, adadza kwa Rehobowamu namuuza kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Kotero anthu anakayitana Yeroboamu ndipo iye ndi Aisraeli onse anapita kwa Rehobowamu ndi kumuwuza kuti, Onani mutuwo |