2 Mbiri 10:18 - Buku Lopatulika18 Pamenepo Rehobowamu mfumu inatuma Hadoramu woyang'anira thangata; koma ana a Israele anamponya miyala, nafa. Ndipo Rehobowamu mfumu anafulumira kukwera pa galeta wake kuthawira ku Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Pamenepo Rehobowamu mfumu inatuma Hadoramu woyang'anira thangata; koma ana a Israele anamponya miyala, nafa. Ndipo Rehobowamu mfumu anafulumira kukwera pa galeta wake kuthawira ku Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Tsono mfumu Rehobowamu adatuma Adoramu amene ankayang'anira ntchito yathangata, koma anthu a ku Israele adamponya miyala mpaka kumupha. Pamenepo, mfumu Rehobowamu adakwera msangamsanga pa galeta lake nathaŵira ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mfumu Rehobowamu inatuma Hadoramu amene ankayangʼanira ntchito yathangata, koma Aisraeli anamugenda miyala ndi kumupha. Koma mfumu Rehobowamu anakwera galeta lake ndi kuthawira ku Yerusalemu. Onani mutuwo |