Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 10:12 - Buku Lopatulika

12 Tsono Yerobowamu ndi anthu onse anabwera kwa Rehobowamu tsiku lachitatu, monga mfumu idanena, ndi kuti Bweraninso kwa ine tsiku lachitatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Tsono Yerobowamu ndi anthu onse anabwera kwa Rehobowamu tsiku lachitatu, monga mfumu idanena, ndi kuti Bweraninso kwa ine tsiku lachitatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Tsono Yerobowamu ndi anthu onse adabwera kwa Rehobowamu mkucha wake, monga momwe mfumu idaanenera kuti, “Mubwerenso kuno mkucha.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Tsiku lachitatu Yeroboamu ndi anthu onse anabwerera kwa Rehobowamu monga ananenera mfumu kuti, “Mukabwerenso kwa ine pakapita masiku atatu.”

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 10:12
4 Mawu Ofanana  

Ndipo tsopano, popeza atate wanga anakusenzetsani goli lolemera, ine ndidzaonjezerapo pa goli lanu; atate wanga anakukwapulani ndi zikoti, koma ine ndidzakukwapulani ndi zinkhanira.


Ndipo mfumu inawayankha mokalipa, popeza mfumu Rehobowamu analeka uphungu wa akuluakulu,


Ndipo ananena nao, Mubwerenso atapita masiku atatu. Nachoka anthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa