Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 10:1 - Buku Lopatulika

1 Ndipo Rehobowamu anamuka ku Sekemu; pakuti Aisraele onse adadza ku Sekemu kumlonga ufumu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo Rehobowamu anamuka ku Sekemu; pakuti Aisraele onse adadza ku Sekemu kumlonga ufumu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Tsono Rehobowamu adapita ku Sekemu. Apo nkuti Aisraele onse atapita kale ku Sekemuko, kuti akamulonge ufumu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Rehobowamu anapita ku Sekemu, pakuti Aisraeli onse anapita kumeneko kuti akamulonge ufumu.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 10:1
12 Mawu Ofanana  

Ndipo Abramu anapitirira m'dzikomo kufikira ku malo a Sekemu, kufikira ku mtengo wathundu wa ku More. Akanani anali m'dzikomo nthawi yomweyo.


Ndipo mfumu Solomoni anali mfumu ya Israele yense.


Onsewa, ndiwo anthu a nkhondo akusunga malongosoledwe a nkhondo, anadza ku Hebroni ndi mtima wangwiro kudzamlonga Davide mfumu ya Aisraele onse; ndi onse otsala a Israele omwe anali a mtima umodzi kumlonga Davide ufumu.


Ndipo mwana wa Solomoni ndiye Rehobowamu, Abiya mwana wake, Asa mwana wake, Yehosafati mwana wake,


Ndipo kunali, atamva Yerobowamu mwana wa Nebati (popeza anali mu Ejipito kumene adathawira, kuthawa Solomoni mfumu), Yerobowamu anabwera kuchoka ku Ejipito.


Nagona Solomoni pamodzi ndi makolo ake, naikidwa m'mzinda wa Davide atate wake; ndipo Rehobowamu mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake.


ndi Solomoni anabala Rehobowamu; ndi Rehobowamu anabala Abiya; ndi Abiya anabala Asa;


Ndipo anapatula Kedesi mu Galileya ku mapiri a Nafutali, ndi Sekemu ku mapiri a Efuremu, ndi mudzi wa Ariba ndiwo Hebroni ku mapiri a Yuda.


Ndipo Yoswa anasonkhanitsa mafuko onse a Israele ku Sekemu, naitana akuluakulu a Israele ndi akulu ao, ndi oweruza ao, ndi akapitao ao; ndipo anadzionetsa pamaso pa Mulungu.


Koma Abimeleki mwana wa Yerubaala anamuka ku Sekemu kwa abale a amai wake, nanena nao, ndi kwa banja lonse la nyumba ya atate wa amai wake, ndi kuti,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa