2 Mbiri 1:7 - Buku Lopatulika7 Usiku womwewo Mulungu anaonekera kwa Solomoni, nati kwa iye, Pempha chomwe ndikupatse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Usiku womwewo Mulungu anaonekera kwa Solomoni, nati kwa iye, Pempha chomwe ndikupatse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Usiku umenewo Mulungu adamuwonekera Solomoni namuuza kuti, “Upemphe chilichonse chimene ufuna kuti ndikupatse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Usiku umenewo Mulungu anaonekera kwa Solomoni ndipo anati kwa iye, “Pempha chilichonse chimene ukufuna ndipo ndidzakupatsa.” Onani mutuwo |