2 Mbiri 1:6 - Buku Lopatulika6 Nakwerako Solomoni ku guwa la nsembe pamaso pa Yehova linali ku chihema chokomanako, napereka pamenepo nsembe zopsereza chikwi chimodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Nakwerako Solomoni ku guwa la nsembe pamaso pa Yehova linali ku chihema chokomanako, napereka pamenepo nsembe zopsereza chikwi chimodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Solomoni adakwera komweko ku guwa lamkuŵa lopembedzerapo Chauta, limene linali ku chihema chamsonkhano, naperekapo nsembe zopsereza zokwanira 1,000. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Solomoni anapita pamene panali guwa lansembe lamkuwa pamaso pa Yehova mu tenti ya msonkhano ndipo anapereka nsembe zopsereza 1,000. Onani mutuwo |