2 Mbiri 1:5 - Buku Lopatulika5 Guwa la nsembe lomwe lamkuwa, adalipanga Bezalele mwana wa Uri mwana wa Huri linali komweko, ku khomo la chihema cha Yehova; ndipo Solomoni ndi khamulo anafunako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Guwa la nsembe lomwe lamkuwa, adalipanga Bezalele mwana wa Uri mwana wa Huri linali komweko, ku khomo la Kachisi wa Yehova; ndipo Solomoni ndi khamulo anafunako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Kuwonjezera pamenepo, guwa lamkuŵa limene adaapanga Bazalele mwana wa Uri, mwana wa Huri, linali komweko kumaso kwa chihema cha Chauta. Ndipo Solomoni adakapembedza kumeneko pamodzi ndi msonkhano wonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Koma guwa lansembe lamkuwa limene Bezaleli mwana wa Uri, mwana wa Huri analipanga linali ku Gibiyoni kutsogolo kwa tenti ya Yehova. Kotero kuti Solomoni ndi gulu lonse anakapembedza kumeneko. Onani mutuwo |