2 Mbiri 1:13 - Buku Lopatulika13 Momwemo Solomoni anadza ku Yerusalemu kuchokera ku msanje uli ku Gibiyoni, ku khomo la chihema chokomanako; ndipo anachita ufumu pa Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Momwemo Solomoni anadza ku Yerusalemu kuchokera ku msanje uli ku Gibiyoni, ku khomo la chihema chokomanako; ndipo anachita ufumu pa Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Motero Solomoni adachoka ku kachisi wa ku Gibiyoni pafupi ndi chihema chamsonkhano, nabwera ku Yerusalemu. Ndipo adalamulira Aisraele onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Kotero Solomoni anabwerera ku Yerusalemu kuchoka kumalo opembedzerako a ku Gibiyoni, ku tenti ya msonkhano ndipo analamulira Israeli. Onani mutuwo |