Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Mafumu 9:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo ndidzalinganiza nyumba ya Ahabu ndi nyumba ya Yerobowamu mwana wa Nebati, ndi nyumba ya Baasa mwana wa Ahiya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo ndidzalinganiza nyumba ya Ahabu ndi nyumba ya Yerobowamu mwana wa Nebati, ndi nyumba ya Baasa mwana wa Ahiya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Tsono Chautayo adzasandutsa banja la Ahabu kuti lifanane ndi banja la Yerobowamu mwana wa Nebati, ndiponso la Baasa mwana wa Ahiya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ndidzachititsa kuti banja la Ahabu lifanane ndi banja la Yeroboamu mwana wa Nebati ndiponso ngati banja la Baasa mwana wa Ahiya.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 9:9
6 Mawu Ofanana  

Tsono kunachitika, pokhala mfumu iye, anakantha nyumba yonse ya Yerobowamu, kufikira adamuononga monga mwa mau a Yehova, amene analankhula padzanja la mtumiki wake Ahiya wa ku Silo;


ndipo ndidzalinganiza nyumba yako ndi nyumba ya Yerobowamu mwana wa Nebati, ndi ya Baasa mwana wa Ahiya; chifukwa cha kuputa kumene unaputa nako mkwiyo wanga, ndi kuchimwitsa Israele.


Nawakantha Yehu otsala onse a nyumba ya Ahabu mu Yezireele, ndi omveka ake onse, ndi odziwana naye, ndi ansembe ake, mpaka sanatsale wa iye ndi mmodzi yense.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa