2 Mafumu 9:8 - Buku Lopatulika8 Popeza nyumba yonse ya Ahabu idzaonongeka, ndipo ndidzalikhira Ahabu ana aamuna onse womangika ndi womasuka mu Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Popeza nyumba yonse ya Ahabu idzaonongeka, ndipo ndidzalikhira Ahabu ana amuna onse womangika ndi womasuka m'Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndithu banja lonse la Ahabu lidzatha phu! Ku Israele adzapha mwamuna aliyense wa banja la Ahabu, kapolo kapena mfulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Banja lonse la Ahabu lidzatheratu. Ndidzachotsa munthu aliyense wamwamuna wa banja la Ahabu kaya ndi kapolo kapena mfulu. Onani mutuwo |