2 Mafumu 9:23 - Buku Lopatulika23 Natembenuza Yoramu manja ake, nathawa, nati kwa Ahaziya, Chiwembu, Ahaziya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Natembenuza Yoramu manja ake, nathawa, nati kwa Ahaziya, Chiwembu, Ahaziya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Apo Yoramu adabwevuka nathaŵa, ndipo adafuulira Ahaziya uja kuti, “Iwe Ahaziya, atiwukira anthuŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Yoramu anatembenuka, nathawa akufuwula kwa Ahaziya kuti, “Ahaziya, anthuwa atiwukira!” Onani mutuwo |
napenya, ndi kuona mfumu inaima pa nsanamira yake polowera; ndi atsogoleri, ndi malipenga, anali kwa mfumu; ndi anthu onse a m'dziko anakondwera, naomba amalipenga; oimbira omwe analiko ndi zoimbirazo, nalangiza poimbira cholemekeza. Pamenepo Ataliya anang'amba zovala zake, nati, Chiwembu, chiwembu.