2 Mafumu 9:16 - Buku Lopatulika16 Nayenda Yehu m'galeta, namuka ku Yezireele, popeza Yoramu anagonako; ndi Ahaziya mfumu ya Yuda anatsikira kukamuona Yoramu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Nayenda Yehu m'galeta, namuka ku Yezireele, popeza Yoramu anagonako; ndi Ahaziya mfumu ya Yuda anatsikira kukamuona Yoramu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Apo Yehu adakwera galeta lake, napita ku Yezireele poti Yoramu anali chigonere kumeneko. Ahaziya, mfumu ya ku Yuda, anali atabwera komweko kudzacheza ndi Yoramuyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Pamenepo Yehu anakwera galeta lake, napita ku Yezireeli, chifukwa Yoramu anali akupumula kumeneko ndipo Ahaziya, mfumu ya ku Yuda, nʼkuti ali komweko kudzamuona. Onani mutuwo |