2 Mafumu 9:12 - Buku Lopatulika12 Nati iwo, Kunama uku; utifotokozere tsono. Nati iye, Anati kwa ine chakutichakuti; ndi kuti, Atero Yehova, Ndakudzoza mfumu pa Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Nati iwo, Kunama uku; utifotokozere tsono. Nati iye, Anati kwa ine chakutichakuti; ndi kuti, Atero Yehova, Ndakudzoza mfumu pa Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Koma iwowo adati, “Iyai ndithu, mutiwuze.” Apo Yehu adati, “Iyeyo wandiwuza mau a Chauta akuti, ‘Ine ndikukudzoza iwe kuti ukhale mfumu ya ku Israele.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Atsogoleri aja anati, “Ukunama! Tiwuze.” Yehu anati, “Zimene wandiwuza ndi izi: ‘Yehova akuti: Ine ndakudzoza iwe kukhala mfumu ya Israeli.’ ” Onani mutuwo |