2 Mafumu 9:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo agalu adzamudya Yezebele pa dera la Yezireele, wopanda wina wakumuika. Pamenepo anatsegula pakhomo, nathawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo agalu adzamudya Yezebele pa dera la Yezireele, wopanda wina wakumuika. Pamenepo anatsegula pakhomo, nathawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ndipo agalu adzamudya Yezebele ku dziko la Yezireele. Palibe ndi mmodzi yemwe amene adzamuike.” Atanena mau amenewo, mneneri uja adatsekula chitseko, nathaŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Kunena za Yezebeli, agalu adzamudya ku dera la Yezireeli ndipo palibe amene adzamuyike mʼmanda.’ ” Kenaka mneneriyo anatsekula chitseko nʼkuthawa. Onani mutuwo |