2 Mafumu 8:23 - Buku Lopatulika23 Ndi machitidwe ena a Yoramu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndi machitidwe ena a Yoramu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Tsono ntchito zina za Yehoramu, ndi zonse zimene adazichita, zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Yuda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ndipo ntchito zina za Yehoramu ndi zonse zomwe anachita, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda? Onani mutuwo |