2 Mafumu 8:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo anachoka kwa Elisa, nadza kwa mbuye wake; ameneyo ananena naye, Anakuuza chiyani Elisa? Nati iye, Anandiuza kuti mudzachira ndithu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo anachoka kwa Elisa, nadza kwa mbuye wake; ameneyo ananena naye, Anakuuza chiyani Elisa? Nati iye, Anandiuza kuti mudzachira ndithu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Pomwepo Hazaeleyo adasiyana naye Elisa, napita kwa mbuyake. Mbuyakeyo adamufunsa kuti, “Kodi Elisa wakuuza zotani?” Hazaele adayankha kuti, “Inuyo muchira ndithu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Choncho Hazaeli anasiyana ndi Elisa ndi kubwerera kwa mbuye wake. Beni-Hadadi atafunsa kuti, “Elisa wakuwuza chiyani?” Hazaeli anayankha kuti, “Elisa wandiwuza kuti inu mudzachira ndithu.” Onani mutuwo |