2 Mafumu 7:19 - Buku Lopatulika19 ndipo kazembe uja adayankha munthu wa Mulunguyo, nati, Taonani tsono, Yehova angachite mazenera m'mwamba, chikachitika ichi kodi? Nati iye, Taona, udzachiona ichi ndi maso ako, koma osadyako ai; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 ndipo kazembe uja adayankha munthu wa Mulunguyo, nati, Taonani tsono, Yehova angachite mazenera m'mwamba, chikachitika ichi kodi? Nati iye, Taona, udzachiona ichi ndi maso ako, koma osadyako ai; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Pamenepo phungu wokhulupirika uja adaayankha Elisa munthu wa Mulungu uja, kuti, “Ngakhale Chauta mwiniwake atachita kutikhuthulira mvula yochuluka chotani, zoterezi nkuchitika ngati?” Apo mpamene Elisa adaamuuza kuti, “Ndithu udzaziwona zimenezo ndi maso ako, koma iweyo sudzazilaŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Mtsogoleriyu ananena kwa munthu wa Mulungu kuti, “Taona, ngakhale Yehova atatsekula zipata zakumwamba, kodi zimenezi zingachitikedi?” Munthu wa Mulungu anamuyankha kuti, “Iwe udzaziona zimenezi ndi maso ako, koma sudzadyako kanthu.” Onani mutuwo |