Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 7:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo iye anaitana alonda ena, ndi iwo anafotokozera a m'nyumba ya mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo iye anaitana alonda ena, ndi iwo anafotokozera a m'nyumba ya mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Tsono alonda apachipata aja adalengeza uthengawo ndipo okhala kunyumba kwa mfumu adaumva.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Alonda a pa chipata aja analengeza uthengawu kwa okhala mʼnyumba yaufumu.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 7:11
2 Mawu Ofanana  

Nadza iwo, naitana mlonda wa mzinda, namfotokozera; ndi kuti, Tinafika ku misasa ya Aaramu, ndipo taonani, palibe munthu pomwepo, kapena mau a munthu, koma akavalo omanga, ndi abulu omanga, ndi mahema ali chimangire.


Niuka mfumu usiku, ninena ndi anyamata ake, Ndikufotokozereni m'mene Aaramu atichitira ife. Adziwa kuti tagwidwa ndi njala, natuluka m'misasa, nabisala kuthengo, ndi kuti, Pamene atuluka m'mzinda tidzawagwira ndi moyo ndi kulowa m'mzindamo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa