2 Mafumu 6:6 - Buku Lopatulika6 Nati munthu wa Mulungu, Yagwera pati? Namuonetsapo yagwera. Pamenepo anadula kamtengo, nakaponya pomwepo, nayandamitsa nkhwangwayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Nati munthu wa Mulungu, Yagwera pati? Namuonetsapo yagwera. Pamenepo anadula kamtengo, nakaponya pomwepo, nayandamitsa nkhwangwayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono munthu wa Mulungu uja adafunsa kuti, “Kodi yagwera pati?” Atamuwonetsa malowo, Elisa adadula kamtengo nakaponya pamadzipo, nkhwangwayo nkuyandama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndipo munthu wa Mulungu uja anafunsa, “Yagwera pati?” Pamene anamuonetsa malowo, Elisa anadula kamtengo nakaponya pamenepo, ndipo nkhwangwayo inayandama. Onani mutuwo |