Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 6:4 - Buku Lopatulika

4 Namuka nao, nafika ku Yordani, iwo natema mitengo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Namuka nao, nafika ku Yordani, iwo natema mitengo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Choncho Elisayo adapita nawo. Atafika ku Yordani, anthu aja adayamba kudula mitengo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Ndipo anapita nawo. Anapita ku Yorodani nayamba kudula mitengo.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 6:4
4 Mawu Ofanana  

Ndipo wina anati, Mulole mupite nafe anyamata anu. Nati, Ndidzamuka.


Ndipo wina analinkudula mtengo nkhwangwa inagwa m'madzi; ndipo anafuula, nati, Kalanga ine mbuyanga! Popeza njobwereka.


monga ngati munthu analowa kunkhalango ndi mnzake kutema mitengo, ndi dzanja lake liyendetsa nkhwangwa kutema mtengo, ndi nkhwangwa iguluka m'mpinimo, nikomana ndi mnzake, nafa nayo; athawire ku wina wa mizinda iyi, kuti akhale ndi moyo;


makanda anu, akazi anu, ndi mlendo wanu wakukhala pakati pa zigono zanu, kuyambira wotema nkhuni kufikira wotunga madzi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa