2 Mafumu 6:2 - Buku Lopatulika2 Mutilole tipite ku Yordani, tikatengeko aliyense mtengo, tidzimangire malo komweko, tikhalepo. Nati, Mukani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Mutilole tipite ku Yordani, tikatengeko aliyense mtengo, tidzimangire malo komweko, tikhalepo. Nati, Mukani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mutilole tipite ku Yordani, tikadule nsichi imodzi-imodzi, kuti tidzakonze malo oti tizikhalamo.” Elisa adayankha kuti, “Chabwino, pitani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Tiloleni tipite ku Yorodani kumene aliyense wa ife akadule mtengo umodzi, kuti timange malo woti tizikhalamo.” Ndipo Elisa anati, “Pitani.” Onani mutuwo |