2 Mafumu 6:11 - Buku Lopatulika11 Koma mtima wa mfumu ya Aramu unavutika kwambiri pa ichicho, naitana anyamata ake, nanena nao, Kodi simudzandiuza wina wa ife wovomerezana ndi mfumu ya Israele ndani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Koma mtima wa mfumu ya Aramu unavutika kwambiri pa ichicho, naitana anyamata ake, nanena nao, Kodi simudzandiuza wina wa ife wovomerezana ndi mfumu ya Israele ndani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono mfumu ya ku Siriya inkavutika kwambiri mu mtima chifukwa cha zimenezi. Choncho idaitana aphungu ake niŵafunsa kuti, “Kodi simungandiwuze pakati pathu pano munthu amene akuthandizira mfumu ya ku Israele?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Zimenezi zinakwiyitsa kwambiri mfumu ya ku Aramu. Mfumuyo inayitanitsa atsogoleri ake ankhondo ndipo inawafunsa kuti, “Kodi simungandiwuze munthu amene pakati pathu pano ali mbali ya mfumu ya ku Israeli?” Onani mutuwo |