2 Mafumu 5:9 - Buku Lopatulika9 M'mwemo Naamani anadza ndi akavalo ake ndi magaleta ake, naima pakhomo pa nyumba ya Elisa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 M'mwemo Naamani anadza ndi akavalo ake ndi magaleta ake, naima pakhomo pa nyumba ya Elisa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Motero Naamani adadza ndi akavalo ake ndi magaleta ake, nakaima pakhomo pa nyumba ya Elisa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Choncho Naamani anapita pamodzi ndi akavalo ake ndi magaleta nakayima pa khomo la nyumba ya Elisa. Onani mutuwo |
Koma Elisa anakhala pansi m'nyumba mwake, ndi akulu anakhala pansi pamodzi naye; ndipo mfumu inatuma munthu amtsogolere, koma asanafike kwa Elisa mthengayo, anati kwa akulu, Mwapenya kodi m'mene mwana uyu wambanda watumiza munthu kuchotsa mutu wanga? Taonani, pakufika mthengayo mutseke pakhomo, mumkankhe ndi chitseko. Kodi mapazi a mbuye wake samveka dididi pambuyo pake?