Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 4:44 - Buku Lopatulika

44 Potero anawagawira, nadya, nasiyapo, monga mwa mau a Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

44 Potero anawagawira, nadya, nasiyapo, monga mwa mau a Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

44 Motero wantchitoyo adaŵagaŵira anthuwo chakudyacho, naadya, ndipo adasiyako, monga momwe Chauta adaanenera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

44 Tsono iye anachipereka kwa anthuwo ndipo anadya china nʼkutsalako, molingana ndi mawu a Yehova.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 4:44
4 Mawu Ofanana  

Ndipo anadya onse, nakhuta; ndipo anatola makombo otsala, nadzala madengu khumi ndi iwiri.


Ndipo onsewa anadya, nakhuta: ndipo anatola makombo otsala madengu asanu ndi awiri odzala.


Ndipo anadya, nakhuta onsewo; natola makombo, madengu khumi ndi awiri.


Pomwepo anasonkhanitsa, nadzaza madengu khumi ndi awiri ndi makombo a mikate isanuyo yabarele, amene anatsalira anadyawo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa