2 Mafumu 4:41 - Buku Lopatulika41 Pamenepo anati, Bwera naoni ufa. Nathira m'nkhalimo; nati, Gawirani anthu kuti adye. Ndipo m'nkhalimo munalibe chowawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Pamenepo anati, Bwera naoni ufa. Nathira m'nkhalimo; nati, Gawirani anthu kuti adye. Ndipo m'nkhalimo munalibe chowawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Tsono Elisa adaŵauza kuti, “Bwerani ndi ufa.” Elisayo adathira ufawo m'nkhali nati, “Apakulireninso anthu chakudyacho kuti adye.” Ndipo adapeza kuti munalibenso zoopsa m'nkhali muja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Elisa anati, “Bweretsani ufa.” Iye anathira ufa mu mʼphikamo ndipo anati, “Perekani chakudyachi kwa anthu kuti adye.” Ndipo mu mʼphikamo munalibenso zoopsa. Onani mutuwo |