2 Mafumu 4:34 - Buku Lopatulika34 Nakwera, nagona pa mwanayo ndi kulinganiza pakamwa pake ndi pakamwa pake, maso ake ndi maso ake, zikhato zake ndi zikhato zake, nadzitambasula pa iye, ndi mnofu wa mwana unafunda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Nakwera, nagona pa mwanayo ndi kulinganiza pakamwa pake ndi pakamwa pake, maso ake ndi maso ake, zikhato zake ndi zikhato zake, nadzitambasula pa iye, ndi mnofu wa mwana unafunda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Tsono adakamgonera mwanayo, nakhudzitsa pakamwa pake ndi pakamwa pa mwanayo. Ndipo m'mene ankadzitambalitsa choncho pa mwanayo, thupi la mwana uja lidayamba kufunda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Kenaka anakwera pa bedi ndi kumugonera mwanayo, pakamwa pake panakhudzana ndi pakamwa pa mwanayo, maso ake anakhudzana ndi maso a mwanayo, ndipo manja ake anakhudzana ndi manja a mwanayo. Pamene ankadzitambalitsa yekha pa mwanayo, thupi la mwanayo linayamba kufunda. Onani mutuwo |