Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 4:32 - Buku Lopatulika

32 Ndipo pamene Elisa analowa m'nyumba, taonani, mwanayo ngwakufa, adamgoneka pakama pake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Ndipo pamene Elisa analowa m'nyumba, taonani, mwanayo ngwakufa, adamgoneka pakama pake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Elisa ataloŵa m'chipinda muja adaona mwana wakufayo atamgoneka pabedi pake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Ndipo Elisa atafika ku nyumbako, taonani, mwanayo anali wakufa atamugoneka pa bedi lake.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 4:32
6 Mawu Ofanana  

Ndipo kunali, zitatha izi, mwana wa mkazi mwini nyumbayo anadwala; ndipo pokula nthenda yake, analeka kupuma.


Ndipo anakwera, namgoneka pa kama wa munthu wa Mulungu, natuluka, namtsekera.


Nawatsogolera Gehazi, naika ndodo pankhope pa mwanayo; koma mwanayo analibe mau, kapena kusamalira. Motero anabwerera kukomana naye, namuuza kuti, Sanauke mwanayo.


Nalowa Elisa, nadzitsekera awiriwa, napemphera kwa Yehova.


Ndipo pamene Yesu anadza, anapeza kuti pamenepo atakhala m'manda masiku anai.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa