Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 4:30 - Buku Lopatulika

30 Koma make wa mwana anati, Pali Yehova, pali inunso, ngati nkukusiyani. Ndipo ananyamuka, namtsata.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Koma make wa mwana anati, Pali Yehova, pali inunso, ngati nkukusiyani. Ndipo ananyamuka, namtsata.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Apo mai wake wa mwana uja adati, “Pali Chauta wamoyo, ndiponso pali inu nomwe, ine ndiye sindikusiyani ai.” Tsono Elisa adanyamuka natsatira maiyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Koma mayi wake wa mwana uja anati, “Pali Yehova wamoyo ndiponso pali inu nomwe, ineyo sindidzakusiyani.” Choncho Elisa ananyamuka natsatira mayiyo.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 4:30
8 Mawu Ofanana  

Ndipo iye anati kwa Yakobo, Dzina lako ndani? Nati iye, Yakobo.


Ndipo Eliya anati kwa Elisa, Ukhale pompano pakuti Yehova wandituma ndinke ku Betele. Nati Elisa, Pali Mulungu, pali inu, sindikusiyani. Motero anatsikira iwo ku Betele.


Ndipo Eliya anati kwa iye, Elisa, ukhale pompano, pakuti Yehova wandituma ku Yeriko. Nati iye, Pali Yehova, pali inu, sindikusiyani. Motero anadza ku Yeriko.


Ndipo Eliya ananena naye, Ukhale pompano, pakuti Yehova wandituma ku Yordani. Nati iye, Pali Mulungu, pali inu, sindikusiyani. Napitirira iwo awiri.


Ndipo wina anati, Mulole mupite nafe anyamata anu. Nati, Ndidzamuka.


Ndipo mkaziyo ananena, Mbuye wanga, pali moyo wanu, zoonadi ine ndine mkazi uja ndidaima pano ndi inu, ndi kupemphera kwa Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa