Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 4:22 - Buku Lopatulika

22 Naitana mwamuna wake, nati, Nditumizire mmodzi wa anyamata ndi bulu mmodzi, kuti ndithamangire kwa munthu uja wa Mulungu, ndi kubweranso.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Naitana mwamuna wake, nati, Nditumizire mmodzi wa anyamata ndi bulu mmodzi, kuti ndithamangire kwa munthu uja wa Mulungu, ndi kubweranso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Tsono adaitanitsa mwamuna wake, namuuza kuti, “Tumizireni wantchito mmodzi ndi bulu mmodzi, kuti ndithamangire kwa munthu wa Mulungu uja, nkubwerakonso.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Iye anayitanitsa mwamuna wake namuwuza kuti, “Tumizireni wantchito mmodzi ndi bulu mmodzi kuti ndipite mofulumira kwa munthu wa Mulungu nʼkubwererako.”

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 4:22
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anakwera, namgoneka pa kama wa munthu wa Mulungu, natuluka, namtsekera.


Ndipo anati, Ulikumuka kwa iye lero chifukwa ninji? Ngati mwezi wakhala, kapena mpa Sabata? Koma anati, Kuli bwino.


Pamenepo anamangirira bulu mbereko, nati kwa mnyamata wake, Kusa, tiye; usandilezetsa kuyendaku, ndikapanda kukuuza.


uthamange tsopano kukomana naye, nunene naye, Muli bwino kodi? Mwamuna wanu ali bwino? Mwanayo ali bwino? Ndipo anati, Ali bwino.


Pamenepo alongo ake anatumiza kwa Iye, nanena, Ambuye, onani, amene mumkonda adwala.


Ndipo popeza Lida ndi pafupi pa Yopa, m'mene anamva ophunzirawo kuti Petro anali pomwepo, anamtumizira anthu awiri, namdandaulira, Musachedwa mudze kwa ife.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa