2 Mafumu 4:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo anakwera, namgoneka pa kama wa munthu wa Mulungu, natuluka, namtsekera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo anakwera, namgoneka pa kama wa munthu wa Mulungu, natuluka, namtsekera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Pomwepo mkazi uja adanyamula mwana wake nakwera ku chipinda cham'mwamba chija, nakamgoneka pa bedi la Elisa, mtumiki wa Mulungu uja, nkumtsekera momwemo, iye nkutuluka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Mayiyo ananyamula mwanayo nakamugoneka pa bedi la munthu wa Mulungu uja. Kenaka anatseka chitseko iye nʼkuchokapo. Onani mutuwo |