2 Mafumu 4:19 - Buku Lopatulika19 Nati kwa atate wake, Mutu wanga, mutu wanga! Pamenepo anati kwa mnyamata, Umnyamule umuke naye kwa amake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Nati kwa atate wake, Mutu wanga, mutu wanga! Pamenepo anati kwa mnyamata, Umnyamule umuke naye kwa amake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Mwadzidzidzi mwanayo adalira mofuula kwa bambo wake kuti, “Mayo! Mutu wanga ine! Mutu wanga ine!” Bambo wake uja adauza wantchito wake kuti, “Kampereke kwa mai wake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Mwanayo anafuwula kwa abambo ake kuti, “Mayo! Mutu wanga ine! Mayo! Mutu wanga ine!” Abambo akewo anawuza wantchito wake kuti, “Munyamule ndi kukamupereka kwa amayi ake.” Onani mutuwo |