Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 4:18 - Buku Lopatulika

18 Ndipo atakula mwanayo, linadza tsiku lakuti anatuluka kunka kwa atate wake, ali kwa omweta tirigu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Ndipo atakula mwanayo, linadza tsiku lakuti anatuluka kunka kwa atate wake, ali kwa omweta tirigu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Mwana uja atakula, tsiku lina adapita kwa bambo wake amene ankayang'anira anthu odula tirigu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Mwana uja anakula, ndipo tsiku lina anapita kwa abambo ake amene anali ndi anthu odula tirigu.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 4:18
4 Mawu Ofanana  

Ndipo mkaziyo anaima, naona mwana wamwamuna nyengo yomweyo chaka chimene chija Elisa adanena naye.


Nati kwa atate wake, Mutu wanga, mutu wanga! Pamenepo anati kwa mnyamata, Umnyamule umuke naye kwa amake.


Ndipo Elisa ananena ndi mkazi uja adamuukitsira mwana wake, kuti, Nyamuka, numuke iwe ndi banja lako, nugonere komwe ukaone malo; pakuti Yehova waitana njala, nidzagwera dziko zaka zisanu ndi ziwiri.


Ndipo taona, Bowazi anafuma ku Betelehemu, nati kwa ocheka, Yehova akhale nanu. Namyankha iwo, Yehova akudalitseni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa