2 Mafumu 4:12 - Buku Lopatulika12 Nati kwa Gehazi mnyamata wake, Itana Msunamu uja. Namuitana, naima mkaziyo pamaso pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Nati kwa Gehazi mnyamata wake, Itana Msunamu uja. Namuitana, naima mkaziyo pamaso pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pambuyo pake adauza mtumiki wake Gehazi kuti aitane maiyo. Gehazi adamuitana maiyo, ndipo adafika kwa Elisa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iye anati kwa mtumiki wake Gehazi, “Muyitane Msunemuyu.” Ndipo anapita kukamuyitana mayiyo, ndipo anabwera nayima pamaso pa Elisa. Onani mutuwo |