2 Mafumu 4:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo linadza tsiku lakuti anafikako, nalowa m'chipinda chosanja, nagona komweko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo linadza tsiku lakuti anafikako, nalowa m'chipinda chosanja, nagona komweko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsiku lina Elisa uja adafika ku Sunemu, nakaloŵa m'kachipinda kam'mwamba kaja kuti akapumule m'menemo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tsiku lina pamene Elisa anafika ku Sunemu, iye anakalowa mʼchipinda chake chija nagona mʼmenemo. Onani mutuwo |