2 Mafumu 3:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo anati, Tikwerere njira yiti? Nati iye, Njira ya ku chipululu cha Edomu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo anati, Tikwerere njira yiti? Nati iye, Njira ya ku chipululu cha Edomu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono Yehosafatiyo adafunsa kuti, “Kodi tidzere njira iti popita kunkhondoko?” Yoramu adayankha kuti, “Tidzere ku chipululu cha Edomu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Yehosafati anafunsa kuti, “Kodi tidzera njira iti popita ku nkhondoko?” Yoramu anayankha kuti, “Tidzera ku Chipululu cha Edomu.” Onani mutuwo |